Reports that Malawi Parliament has bought four vehicles for leader of opposition Lazarus Chakwera, speaker of parliament, Richard Msowoya and his two deputies, all summing up to K300 Million have prompted commentators to call the officials selfish and inconsiderate.
Billy Banda, one of the commentators in the country said there was no need for government to buy the vehicles for the officials as the country is going through economic hardships.
“Government should have addressed the problems facing the country before buying the vehicles for the officials,” said Banda.
He further said that this shows that the officials are not considerate even though donors are not supporting the country and Malawians are being affected by hunger.
However, Public Relations Officer for Parliament Leonard M’mengezi said the speaker will hold a media briefing on Thursday to clarify the issue.
He further said that he is puzzled as to why the matter has come out now when the vehicles were purchased in the last financial year.
u pipo bwanji? akanakhala kuti magalimotowa anagulilidwa ndi anthu aboma mmmmmm
acakwela asakopeke ndizopusazo iyo apitilize chilungamo cao ba kt 2019 ASAZAKUMANESO NDI ZOVUTA
Mtsogoleli wokalamba kwambiri Ali ngati mwana ndipo ukalamba sumaona ma degree ayi amalawi kk
Kkkkkk Malawi osauka koma anthu onjoya …..ndimadabwa kuti a busa kusiya mpingo kumalimba ndi ndare za chopereka zimawachepera relo akufuna kuononga dzulo awa kkk
Man zikuwoneselatu kt it wz nt a calling from God….cz mulungu akakuyitana samasitha kt pano basi mwandigwirira ntchito kapangeni zina…noooo..de bible says he is nt a son ov man that he can change his mind
anthu mukunenao ndi ogulilidwa,bwanji dpp idasankha kutelo osakapeleka ndilamazo kuntchito zina.
wawagulira ndani mmesa boma linaletsa kugula magalimoto atsopano even ma cabinet ministers akukwela akale bcz of that ban
palibe wabwino apa.takumana okhaokha adyera.
This is an uprising of the power against the Politician ,things start very small like ka mbeu ka mpilu ,these poor pipo are holding anger in their heart ,study how RENAMO was founded ,these pipo can fight without giving them money ,they are tired of poverty ,seeing you driving expensive vehicles ,I remember a certain president of Brazil was using a VW bittle was loved by all ,
Government bought this Car Reg # LL 1, for Mayor who used to sleep all the time.
Amene angadane Chakwera n Msowoya ndi mbuli and samaziwa ndale za dpp akufuna tiiwale UNGA SAGA iwo akhale a bwino angokoza mavuto a iyeyo ndi vice malawianz knwz de truth.
Ma Prado akukwera ndani? Mukukwera ma Prado anthu alibe mankhwala muzipatala? Ma supporters anu akuyenda ndi zigamba, akugonera mango? Inu ma Prado mukunyamuliramo zibwezi zanu, ana anu? Dziko losauka ngati Malawi wina ndikumayendera Prado? Pamene kumudzi kwathu kulibe mseu, bridge. Prado ili ndi ma tank awiri a mafuta. Tank imodzi imalowa 45-55 litres. Mukuyendera ku campaign, kupita ku tchalitchi ku kampeni, ma tyre a Prado limodzi ndi K700,0000. Ndipo ikamayenda yenda, muyenera kusintha, every 6 months. Ma Prado amenewo agulitsidwe, makobili ake
anagula prado ndani mesa ndi boma ziti anthu akuvutika bomalo silinadziwa kodi ma prado ukunenawo analembedwa msowoya kapena chakwera mesa analembedwa mg ina parliment1 meadziwa liti zoti ndalama zawonongeka pogula magalimoto magalimotowo agulidwa liti mukulankhula lero inu mudziwanu ndiliti unapita ku smerica ku kasakaxa ndalsms kumalingslila poyankha wanva iwe
a busa ndi a Vice awo agwa m’mayeselo adyela kkkkkk nanga mayeselo adziko mungalimbe? e.g ma Demo!
Iwe chakwela ukanakhala wa dzeru sukadasiya kupanga za uzimu mulungu adachoka mwa iwe kalekale.Oposition leader wake adatembeleledwa ndipo dzeru zidatha
Nde kuti za chimanga ayi koma galimoto ndikanakhala inetu za magalimoto mkanadikila njala iduse kaye
Dziko la Malawi lidzavutika mpaka kale..utsogoleri okozako Malawi kukhala bola sadzapezeka..amalawi omwe adapita ku xool ndiambiri koma nzeru ndi mphamvu ya utsogoleri kulibe..amakhala ngati mphamvu ya utsogoleri ndi nzeru amakhalira
It is th foolish DPP.
2 divert the UNGA saga kodi za hayala ya ndege simukunena bwanji? & magalimoto anagulidwa miyezi yapitayo osati panopo malopota kudya chiponda kkkk
2 divert the UNGA saga kodi za hayala ya ndege simukunena bwanji? & magalimoto anagulidwa miyezi yapitayo osati panopo malopota kudya chiponda kkkk
ndikuganiza kuti ndibwino kupeleka coment rather kuwatukwana anthu a chikulire ngati amenewa. my yaweh is watching u remember.
agalu inu mwatifasira kutidyera misonkho yathu wokuba inu !!!
Kkkkkk,Chakwera vs APM
Mbuzi
Chakwera is possed en needs deliverance,,,,were is Jessy fluid kabwira??kkkkkk
mwamuwona bwanji?mtsogoleri wa MCP
at least tapumako za bushiri
Parliament proposed the purchase of three vehicles, government release the funds, now u r saying MCP ibweze ndalama kupusa basi, lero mwapanga fund ma demo ndalamazo mwatenga kuti? Sikomwe munatenga zamagalimotoko agalu inu
onsewa dey r selfish.palibe man of God in politics.dc remains a dirty game
Anation full of stupid media insitutions, stupid opposition etc…do we need to xool u fools that parliament being an independent arm of gvt it budgets and procure resources including vehicles??..DO we need to civic educate u idiots that chindere msowoya as incharge had the power to stop any extra vagant shoping considering the current economic situation as observed by prostitute Kabwila when he she xool gvt on the same following the UN trip??..Imean iz it not Stupid chakwera who neary cried at arally in the north just recently when he was lamenting abt the UN trip…?..indeed stupid everything including so called mcp_activists who hv brided poorly paid so called journalists trained @ Ntchenantchena.college …….to write and make noise against gvt…..Shame on u….Supporters of DPP will not vanish into the air as easy as u may daydream….Fools!
ih mukungoonongabe ndalamazo?
Trip ya us imakupwetekani eti kkkkk mukanapita nawo mukanadandaula kaya
wakawaka hotel jessey nd chakwera!2:30pm1000 per heldC U DEA
I thought those vehicles are bought by government like ministerial ones. Why putting the blame on Chakwera n Msowoya? DDP propagandas will never end. Konseko kuti mwina tiiwale za ku USA zija. Mwatchera ku mwezi nkhanga zaona kale.
govt banned the purchase of vehicles bt parliament dified that order through the speaker
Bro the ban is for 2015 to 2016 budget n those vehicles were on 2014 to 2015 budget which was approved by finance minister and those vehicles arrived in january 2015 why now.
God shid intervene 4pple 2b opened their eyes
Wanzeru ndi Lucius Banda yekha muyumba yonse ya malamulo, enawa ndi manyaka enieni!
#UMBULI siwabwino, & mbuli kut imvetsetse sichapafupi,, #vehicles r not in de name of mcp, but government, and in parliament #mps do discus & agree the issue discused,,, why u r insultng innocent pple like #chakwera, msowoya and others? this is plan of government,,, ANTHU osazindikra amangotukwana basi, shit!!!
Those commentators are stupid. Who is selfish between the one who provided money and the one who used it. musatinyase apa.
panya pao mbamva inu
Ma CSo panganitu ma demo tiwone chilungamo chanu apa!!
Guyz! What the hello z Maejor John Gunde & Kind of this blue mbuzi Maejor & his senseless shit talk about the main opposition leaders. Pariamentary Cars are not for Dr.Chakwera & His Right Hon. Msowoya. Those Vx Vehicles belong to Parliament & the Govn of the time & very same vx cars will ever be used by very govt either by Ngwazi Dr.Lazuras Chakwera Or the same teethless blue fox president come 2019. So whats the matter you coacoroch?. Damn Shit!
Dont start with Chakwera,the bigman there is the Speaker,deputy,vice deputy then Chakwera,why are you jumping to him and why not asking about the chattered jet and m’dipiti of people to UN in USA? All you want is to chop the money yourself,let others mis use too you started it yourself and Chakwera didnt demand for acar he was offered acar just like the secretaries were offered to USA they cldnt say no same to Chakwera.
Kodi poyamba amakwela chani? Ulemelero wapadziko lapansi. Anzao akuvutika. Otsutsawo osakana bwanji? Anthuwa ndiamodzi basi!
anthu onseo agulilidwa ma galimoto ndi mbuzi komaso wagulayo ndi chitsiru coz akuwaphimba m’maso, tsiku lina adzawakumba. atengere chitsanzo kwa amai, masten akulephera kubwera kwao chifukwa cha ndege. amalawi kusaphunzira, that’s why anakunenani kuti ” agalu inu”. amene uja anaona kuti mu Parliament mulibe anthu koma agalu.
Chauta akuoneni mwapaderdera nonse
Damn shit blood furken foxes commentators & that ur blue teethless president & his cabnet misters are all the bird brained politiciats. There z no way u can start blaming Parliament with those four Vx Vehicles without getting to the botton of that tripple stupid New York Extravaganza. Challenge Me, Mr. Ruler!. When was the blue Big Goat publicly announcing the nation about his cocoaroch which gone to UN G.Assembly with their feck blue teethless boss? & on that again, Who sponsored his 115 feck people entourage to UN General Assembly? Dpp Apm hired a 300 million jet from abroad & that blue Goat extravagantly spent the tax payers funds amounting to 1. 5 billion Mk for accomodation, delicious food, transport & the like. Instead, Dpp Apm the big goat & his coacoroch commentators have foolishly opted for a stupid propaganda to divert the true people’s attention on that serious hot issue. What Hello are you Dpp Apm?. Dp
Achakwela makani onse balala angakuleso mtima pamenepo siamugula basi zimenezo nde ndale zapanyasalande kkkkkkkkkkk
Azdya akudyera xool yawo
ndiye zamasiku ano zimenezi tiyeni tizingoziona
Kkkkk….kkkkkk…ndikuseka ngati za bwino koma no …John Gunde tauze mmene zaku mnyasira mwina sakumvesa……kkkkkk.
ahhh adziyenda pansi? jealous Bwanji. forgetting cashgate chakweate
siufa mumati peter aziyenda pansi kupita ku UN.
Parliament imeneyi. Foolish pipo. Pantumbo pawo achina chakwera ndi nsowoya wako. Anamachende inu
Kkkkkkkkk achimwene nde mumakwiya2
iii athu amenewa andikwiyisa heavy.
nyapapi magalimoto wagula ndi muthalika ndi Dpp kuti apatse anthu ukuwatukwanao.ogula ndi opatsidwa olakwa ndani,zinazitu kumavetsetsa musanakomente,mukutichititsa nazo manyazi.
iwe pakholopako wamva? Pamnyero pako. comenti yaine chakukhunza ndicha? Machende ako. Ukundiputa dalatu ulandila maphuzo. Pamtudzu pako wamva?
bwanji ndikupitile pa wall pako? Samala namachende iwe. Pamnyini pako.
Buying vecals 4 leaders of oporstion ok to me it looks like tramp take care chakwela and ur frends
SELFISH INDEED
selfish indetu
Achakwela akadakhaladi abuse akdathandiza anthh
Palibe wabwino
kodi boma muzigula magalimoto odula pamene a2 kumuzi akufa ndi njala? day 1 u will never mu2 womulamulira onse atafa ndiye muzizalamulira azimbwiyanu? aDog
Chakwela nayenso ndimbuzi yamunthu bax sindizamvotela akungoti phimba mmaso
That is the senseless following the the situation we’re.
eee zanu izo
They r selfish n egoists indeed coz instead of allocating that fund 2 other areas, i mean ministries who r struggling in their operations Due 2 lack of money they r just squandering or embezzling directly on indirect so no matter hw we cn try 2 voice out our concerns to them, it won’t yield anything but tym wil come when they need us most campaign period
Akungotchulidwa speaker ndi chakwera bwanji? What about mcheka chilenje and chiwaya
THEY R THE HEADS
eti inu… dpp,udf,mcp onsewa ndi makape…samaganiza bwino..they dont walk the talk…samitsiru…andibowa
mmmmm mwachita bwino kwagulira magalimoto
Akukwerabe zanu
The problem is not the one driving the car, but the one buying the cars coz they know very well that Malawi’s economy is not that stable but still they are buying very expensive cars.. This is madness at an advanced level..