Eight Malawi Defence Force (MDF) soldiers were yesterday involved in an accident which claimed the life of one of the soldiers.
A Malawi Defence Force bus registration number MDF 1455 was travelling from Lilongwe to Blantyre when the back tyre burst at Nkhande and the driver failed to control the bus.
Speaking to one of the local radio stations, police confirmed the death of the soldier and identified him as Bruno Nkhaya aged 37 who was working at Kamuzu Barracks in Lilongwe.
The other seven sustained different injuries and are currently receiving treatment.
Poleni sana
if t z police officer achita bwino agalu amenewa alibe ulemu koma ngat nd mdf mmmm Rip
Kodi amalawi 24 mumaphunzira kuti? Mdf mukukayika za a police muzanenapo zoona inu?
Za nkutu.
This is so bad.R I P
R I P.
Sizikugwirizana…….
Sizikugwirizana…….
Akulu chemagwira ndipemphero langa kuti inuyo ngati muli ndi bale wanu omukonda amwalire posachedwapa olo inu amene mutamwalira, imfayake achiwembu akukhapeni kuti mumve kuwawa caz of your stupit comment
Iwe 24 umakamba nkhani zabodza bwanji? Tanena police or Mdf
I thnk nkhani zanu zumakhala zoona
Mwatha maplan
Driver wamangidwa mmene amapangira ma driver ena onse? tell us the truth here.
auze kuti akufawo azilemberapo ena kuumila bwanji
sorry to MDF for their loss.
pa barlworld apa opposite kamuzu stadium koma inu bodza za mlakanso mwaika pic yabodza
Sad News..R.I.P
Xory, xory neighbour RIP
R I P
R I P
R I P
Uku ndiye kusocheletsa ntundu wa anthu
Police officer or mdf tanenan chimodz timve malawi 24
Oh this is a very sad news may the almighty god do take care of them, but may you collect yr english we dont say back tyre but rear tyre. Sorry for this
I passed by Nkhande on ma we to Boma….just 15 mins afta de accident…but was it back tyre that burst??? Not front driver’s side tyre????? Mmmmmm mwina nnalakwa kuona…but MALAWI24 mmmmmm kumafufuza bwinobwino…….
Malawi 24 mbuzi inu kuzolowera kunamiza anthu……shupit! ;(;(;(;(;(
kkkkkk if its true RIP koma ndikuonatu chimbaula osati bus
Is this the accident or police vehicles doing the patrol?
eeh koma pic iyi mumaikondatu zitsiru inu
natural selection R.I.P mawa ndi iwe ndi ine may gud LORD comfort our heart.its so painful to loose our soiders
Un professionalism Malawi 24
zomatipusitsa ife ayi coz ife c ana
Gud News
RIP FF
RIP Officer.
a souldier never die!I read from somewhere else
tikukupemphani kuti mukalemba nkhanizi muziyesesa kuyika chithunzi chazinthu zachitikazo plz ngati mulibe ingolembani popanda chithunz plz
Your posting police officers why not MDF?malawi 24 plz wakeup if dot not have full information dont post anything.we are in the world of techno now
Techno is a kind of music dude
Sorry
Ku Malawi tikugonabe picture mwaika apa siya bus yasilikali ayi ndi yapolice zakalekale izi please be updated dziko linasintha ili.
kkkk angayandikire kukajambula a MDF
Rip
Pepani za ngoziyi
SEE U IN GRACE LAND SOIDIER AS WE ALSO BELIEV IN LIFE AFTER DEATH AND WE ALSO STRONGLY BELIEV U ARE IN JAHOVAHS ARMY NOW…REST IN PEACE SOIDIER
Tiyeni kumaliro tikaone kuomba kwa mfuti
RIP Soldier
Ndimene zmakhalira
sorry thats bad news,
Ndie picture ndi a police sizukugwirizNa mukukambazi
R .i .p
Oh sorry,our soldier,rest in peace.
sorry my bra. rest in peace
Picture mwayikayo ndi yah PMS or MDF?
…very sad, I saw this bus parked @ Ntcheu boma opposite Peoples Supermarket.
zosakomaaaaa
So this is every day picture to show when u got news about police and mdf? You are lazy to go out there and capture real things huh?
RIP to the soldier
So why putting police vehicles there huh?
RIP!!
R.I.P
R.I.P Buddy
Amachitira matama anthu amenewa tikaonana moyo winawo
Man Aliyense amapanga matama!
Man,imfa aliyense adzayiwona nde zamatama ponyani uko. Just say RIP mwina iweyo ndi mawa lino
Man #Drake munayambapo mwakumana nd nkhanza zomwe amapanga anthu amenewa?
I kno them well man Mjura. Komabe imfa ikafika kwa nzathu paja olo amfumu mmudzi amati kwanga nkulira kuti ndataya munthu ofunika kwambiri pomwe malemuyo inali mbava yotheratu man
Moto umapita kwatsala tchire usamakambe za wina atafa
Inu poti mulibe matama, i think ndinu amuyaya
Mjura Magwira i think your brain has virus coz normal capable thinking person can not say that i dont brame you but your sickness of the brain i kno where you r so mind your language.
ndinu amuyaya
Mawa ndi mbale wako udzawawona matamawo!
Kkkk kma Picture imeney nde mumaykonda2 kulibe ina eeeish yatopesa iyy any way Rip soulja
zoxakhala bwino
Very bad indeed may the soul of the deceased rest in ertenal peace
Sorry.
rip buddy
Sorry 4dat
bad news for our security forces
Rest In Power SoldierMan
so sorrowful.RIP.
so sorrowful
so bad. May God comfort the bereaved family.
may hiz soul R.I.P