Achinyamata khumi ndi awiri awathamangitsa ku Israel
Achinyamata khumi ndi awiri omwe anayiwala kuti ukayendera n’zengo usati asakhwi afumbura, awathamangitsa m’dziko la Israel kamba kotaya chingamu chifukwa cha mtedza olawa. Sabata latha, a Polisi m’dzikolo anamanga achinyamata okwana makumi anayi ndi mphambu… ...