Kupweteka kwa Thandi Galeta kunatisokoneza, watero mphunzitsi wa Malawi
Mphunzitsi wa timu ya mpira wa manja ya Malawi Samuel Kanyenda wati kupweteka kwa Thandi Galeta kunasokoneza timuyi lero pa masewera ake ndi Uganda. Uganda yasambwadza Malawi ndi zigoli 57 kwa 46 lero masanawa mu… ...