
Ndirande ilowa m’bwalo mawa
Ochita malonda ku Ndirande mu nzinda wa Blantyre alengeza kuti mawa achita ziwonetsero posakondwa ndi kukwera mitengo kwa katundu osiyanasiyana zomwe akuti zakhuda malonda awo. Wapampando wa ochita malonda mu nsikawu, Chancy Widon, wauza nyumba… ...