
Tili pa mavuto chifukwa atsogoleri sakudziwa chochita – Kabambe
Yemwe anali gavanala wa banki yayikulu ya Reserve a Dalitso Kabambe, wati dziko la Malawi likudutsa m'mavuto adzaoneni chifukwa choti linasankha ndikuyika anthu m'maudindo omwe sakudziwa choyenera kuchita. Kabambe yemwe ndi m’modzi mwa anthu… ...