Saulos Chilima - Lazarus chakwera

Ndinali mboni – JB

Mtsogoleri wakale wa dziko lino, Joyce Banda wati pa mgwirizano wa Tonse Alliance, iwo adali mboni pamene mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera ndi wachiwiri wawo wakale malemu Saulos Klaus Chilima amagwirizana kuti aliyense adzalamulira… ...