
Chaka chino ndi cha masankho, tilimbane ndi kuchotsa njala ilipoyi – Msusa
Archbishop wa mpingo wa Katolika mu Archdiocese ya Blantyre, a Thomas Luke Msusa ati chaka chino pokhala chaka cha masankho aMalawi akhalebe aMalawi ndipo alimbane ndi kuchotsa njala ndi umphawi zomwe zakuta dziko lino. Poyankhula… ...