Zamkutu! Gwengwe wati a Malawi ayiwale za K7 thililiyoni ya Bridgin
Pomwe anthu anali ndichiyembekezo kuti zinthu zambiri zitha kuyamba kuyenda bwino kaamba ka ndalama yokwana K7 thililiyoni yomwe bungwe lakunja la Bridgin Foundation limayenera kupeleka ku dziko lino, nduna ya zachuma a Sosten Gwengwe athira… ...