Tchimo langa ndikukhala mpondamatiki wa ku Malawi, watero Bushiri
M'modzi mwa aneneri otchuka mdziko muno yemwe anamanga maziko ake ku South Africa, mneneri Shepard Bushiri wati tchimo lomwe limamupangitsa kukhala oyipa m'dziko muno ndi kukhupuka. Mneneri Bushiri wati anthu ochuluka Ku Malawi kuno amamuda… ...