Bushiri wagawa chimanga ku mawanja okhudzidwa ndi madzi osefukira ku Mangochi
Pomwe miyanda miyanda ya anthu omwe amakhala mphepete mwa nyanja ya dziko lino akhudzidwa ndi vuto lakusefukira kwa madzi, mtsogoleri wampingo wa Enlightened Christian Gathering, mneneri Shepherd Bushiri wagawa chimanga ku mawanja okhudzidwa oposa 200… ...