Tisunga bata mpaka liti pomwe ana athu akungotha? – Yalira Inkosi Kwataine
Inkosi Kwataine ya m’boma la Ntcheu yadandaula kuti anthu opeleka chiyembekezo ochokera m’bomali amafa mosadziwika bwino ndipo ati ndiodabwa kuti anthu akuuzidwa kuti asunge bata pamene imfa ya yemwe anali wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko… ...