
Mbama yoyera: Papa akuntha mzimayi
Papa Francis anakuntha dzanja la mayi wina yemwe anamukoka Papayo ku chisangalalo cha chaka chatsopano ku St. Peters Square. Izi zinachitika lachiwiri Papa, yemwe ndi mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse, atangomaliza kumupatsa… ...