
Nane ndili ndi mafunso ochuluka – JB
M'tsogoleri wakale wadziko lino mayi Joyce Banda, wati iyenso ali ndi mafunso ochuluka zedi pa zomwe zinachitika pa tsiku lomwe wachiwiri wakale wa m'tsogoleri wa dziko lino malemu Saulos Chilima anafa pa ngozi ya ndege… ...