
Zamanyazi: Chakwera wanamiza mtundu wa Malawi, ku Phalombe sikunamangidwe nyumba 29 za Polisi
Zadziwika kuti m'tsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera lero wanamiza a Malawi ku nyumba ya malamulo pomwe anati Boma lake la kongelesi lamanga nyumba 29 za a Polisi mu m'boma la Phalombe. Koma khonsolo ya… ...