Bwalo lisekelela odula ziwalo zobisika: awagamula zaka zisanu zokha
Anthu awiri amene amapha anthu ndi kuwadula ziwalo zawo zobisika kuti akazigulitse, achoka ndi chimwemwe kutsaya pamene anatengeledwa ku Khoti mu boma la Nkhotakota. Malinga ndi ma Lipoti, abambo awiriwa anamangidwa atapita kukatsatsa malonda awo… ...