
NAM yakhutila ndi luso latsopano lomwe yapeza
Bungwe loyendetsa masewero a mpira wamanja mdziko muno la NAM, lati ndilokondwa ndi luso latsopano lomwe lapeza mmadera osiyanasiyana. Mlembi wamkulu wa bungweli, Yamikani Kauma wayankhula izi lero pa bwalo la zamasewero la Bingu, mumzinda… ...