
Apolisi ati mipingo ili ndi udindo wolangiza akhristu zakuyipa kodzimangilira
Apolisi mu boma la Machinga apempha amipingo kuti pamene akulalikira mau a Mulungu kwa akhristu awo, asamalepherenso kukamba nkhani zokuyipa kwa imfa zobwera chifukwa chodzimangilira komanso kuyipa kwa kulanga okha munthu yemwe akuganiziridwa kuti wapalamula… ...