Aphunzitsi ena ku Thyolo sanalandilebe ndalama atayang’anira mayeso a JCE
Aphunzitsi okwana 59 m’boma la Thyolo adandaula kuti bungwe loyendetsa mayeso la MANEB silikuonetsa chidwi chowapatsa ndalama zawo za alawasi pa ntchito yoyang'anira mayeso a JCE, pomwe anzawo ena analandira mayesowa asanayambe kulembedwa. M'modzi mwa… ...