Yalakwa! mafuta akweranso mtengo, ma minibus nawo ali m’mbuyomu
Patangodutsa masiku owerengeka chabe boma la Malawi litakweza mitengo ya mafuta a galimoto, mitengoyi yakwezedwaso. Izi ndimalingana ndi chikalata chomwe chatulutsidwa lachitatu ndi bungwe loyang'anira mafuta m'dziko muno la Malawi Energy Regulatory Authority (MERA). Malingana… ...