Asilikali awiri apamadzi sakupezeka ku Mulanje
Asilikali awiri omwe amafuna kupulumutsa anthu ena omwe akhudzidwa ndi madzi osefukira m’boma la Mulanje, sakupezeka. Malingana ndi nduna ya za ma boma a Richard Chimwendo Banda omwe ali pa Mkando m’boma la Mulanje, asilikali… ...