
M’busa amwalira pamene amazibatiza yekha
M'busa wina mu nzinda wa Lilongwe wamwalira pamene analowa mu m’tsinje wa Bua kuti azibatize yekha. Zadziwika kuti m’busayu dzina lake ndi Chisomo Duncan wa mpingo wa Ziyoni ndipo anapita kukabatiza nkhosa zake mu mtsinje… ...