Tibaye nawo galu – wamangidwa ku Lilongwe kamba kogulitsa kanyenya wa galu
Ngati muli bwenzi wa ziwaya za nyama mu Lilongwe, ndi kutheka munadya kale galu wanu. Maka anthu amene mumakonda kubaya ya mbuzi. A polisi mu mzinda wa Lilongwe amanga bambo Andrew Mthiko a zaka 38… ...