
Bambo ogulitsa makala wamwalira atagwera mutsinje pomwe amathawa achitetezo
Bambo wina, Yamikani Kawala wa zaka 28, yemwe amachita malonda ogulitsa makala, wamwalira atadumphira mu mtsinje pofuna kuthawa a chitetezo a nkhalango atakumanizana naye ali ndi matumba awiri a makala. Malinga ndi mneneri wa polisi… ...