Apolisi akusakasaka dalaivala yemwe analanda mfuti ya wapolisi
Apolisi mu mzinda wa Lilongwe akusaka dalaivala wa truck, Grey Chisinga, yemwe akuti analanda mfuti ya wapolisi wina pa nthawi imene apolisi anamanga dalaivalayu pa mlandu ozembetsa feteleza. Wachiwiri kwa mneneri wapolisi ku Central West… ...