
Khonsolo ya mzinda wa Lilongwe ipereka chilolezo ku chipani cha DPP
Khonsolo ya mzinda wa Lilongwe yapereka chilolezo ku chipani cha Democratic Progressive (DPP) kuti chipanichi tsopano chitha kuchititsa misonkhano yoyimayima m'madera ena a mu mzinda-wu. Izitu zikudza pamene pangodutsa nthawi yochepa khonsoloyi itakana pempho la… ...