
Chakwera ndi m’farisi – atelo a Boma
A Boma komanso a chipani cholamula atopa naye mtsogoleri wa Kongeresi Lazarus Chakwera moti ayamba kumuvula pagulu. Akulualuku a chipani cholamula cha DPP anamemeza atolankhani mu mzinda wa Lilongwe pamene anayamba kumumasula mtsogoleri wa zipani… ...