Makolo, ophunzira, agenda aphunzitsi kamba kakukomoka kwa ana atatu
Chipwilikiti chinabuka pa sukulu ya pulayimale ya Chingale m'boma la Zomba pomwe ophunzira atatu adakomoka mosadziwika bwino Lachitatu m'mawa. Izi zitangochitika, ophunzira komanso makolo ena okhudzidwa anayamba kugenda aphunzitsi ndi sukulu ati chifukwa chokwiya ndizomwe… ...