A Malawi mumva kuwawa – Chakwera
Pulezidenti wa dziko lino Lazarus Chakwera wati aMalawi amva kuwawa kwa miyezi ikubwerayi potsatira kugwa mphamvu kwa ndalama ya Kwacha. A Chakwera ananena izi usiku wa lachitatu pomwe amayankhula kwa mtundu wa aMalawi kuchokera ku… ...