
Kukwera kwa mtengo kwa tomato kwakhudzaso anthu ogulitsa
Anthu ochita malonda ogulitsa tomato mu msika waukulu mu mzinda wa Blantyre adandaula kamba ka kukwera kwa mitengo yowodera tomato zimene zikuchititsa kuti bizinezi yawo ilowe pansi. Modzi mwa anthu ochita malondawa, Christopher Gama wati… ...