
Malawi sakukwanitsa kusamalira atsogoleri ake akale – atero a Bakili Muluzi
Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Bakili Muluzi ati chisamaliro cha atsogoleri opuma chomwe boma limapereka chikufunika kuunikidwanso, ponena kuti pali zigwelu zambiri zofunika kukonza . Mtsogoleri wakaleyu wati, mwa chitsanzo, pakali pano amagwiritsa ntchito… ...