Chakwera akufuna kuchotsa Chizuma kudzera mwa anthu ena – Kalindo
...wayitanitsa zionetsero ku Mulanje A Bon Kalindo ati zomwe zikuchitika pankhani yakumangidwa kwa mkulu wa ACB a Martha Chizuma, ndi chinyenga aphunzitsi ndipo ati zili ngati mfiti yomwe imamupha munthu ndipo yomweyo imakaliraso kwambiri pa… ...