![Malawi Dorothy Shonga](https://i0.wp.com/malawi24.com/wp-content/uploads/2024/04/Dorothy_Shonga_Zeze-Kingston-e1713527860206.jpg?resize=235%2C176&ssl=1)
Wakamang’ala ku bwalo Doro wa Zeze: anandinamizira kuti ndinakwera bus pomwe ine ndinakwera ndege
Kulitu nkhani ku bwalo uku. A Easter Gondwe omwe amatchuka ndi kukamba nkhani pa tsamba lino la Facebook akasumilidwa. Doro wa Zeze ndiye wakamang'ala kuti a Gondwe ndi a 'hater' ndipo amamudyola kwabasi. Akufuna abwalo… ...