
Aliyense atengepo mbali polimbana ndi ziphuphu ndi katangale – Chizuma
Mkulu wa bungwe lolimbana ndi kuthana ndi mchitidwe wa ziphuphu komanso katangale la Anti-corruption Bureau, mai Martha Chizuma, ati ndi kofunika kugwirana manja kuti dziko lino lipambane pa nkhondo yolimbana ndi mchitidwe oipawu. A Chizuma… ...