Chule anakana m’madzi muli mwake: a Matola ati a Malawi atanthauzira molakwika mwambi wawo
Pamene anthu akupitilira kukakamiza nduna yowona za mphamvu ya magetsi a Ibrahim Matola kuti apepese pazomwe anayankhula dzulo m'boma la Dedza, a Matola ati anthu sakutanthauzira bwino mwambi omwe iwo anapeleka. A Matola akudzudzulidwa kaamba… ...