A Malawi oposa 200 akupita ku Israel kukagobola
Ndege yomwe ikuyembekezeka kunyamula a Malawi oposa 200 omwe boma likuti lawapezera ntchito m’dziko la Israel, yafika kale m’dziko muno ndipo anthuwa anyamuka pakati pausiku lero. Ndege yonyamula anthuwa yomwe ndiya aRKIA Airbus a321-251NX, inatela… ...