Osamatiopseza ndi mavoti anu – Chilima
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, a Saulos Chilima, ati a Malawi asiye kuliopseza boma ndi mavoti awo. Iwo anena izi ati ngati munthu wamba pothirapo ndemanga pa mkumano wa bungwe la anthu otsata zachuma… ...