Wayamba kampeni Mutharika, ali pa Njamba mawa lino
Mtsogoleri wa chipani cha DPP, a Peter Mutharika amene owakonda amangoti APM, akuyembekezereka kugwedeza mzinda wa Blantyre mawa lino pa 12 May. A Mutharika amene akhala nthawi osachititsa msonkhano wandale alengeza kuti akhala pa Njamba… ...