Wa polisi wanjatwa kamba koba foni ya mlonda
Wa polisi wa zaka 41 ku Ulongwe m’boma la Machinga ali m'manja mwa apolisi anzake kamba kakuba lamya ya m’manja ya mlonda wina. Malingana ndi lipoti lochokera pa polisi ya Liwonde m’boma la Machinga, omangidwawa… ...