Ogwililira azimenyedwa kaye – nduna yazachitetezo
Pomwe dziko la Malawi lili mkati mopeza njira zothanilana ndikukula kwamchitidwe ogwililira, yemwe ndinduna yowona zachitetezo m'dziko muno a Richard Chimwendo Banda awuza anthu kuti azimenya wina aliyense opezeka atagwililira. A Chimwendo Banda amayankhula izi… ...