Mutharika akana kusainira malamulo achisankho, kuchotsa makomishonala a MEC
Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika akana mwa ntu wagalu kusainira kusintha kwa ena mwa malamulo oyendetsera chisankho m'dziko muno. Izi zadziwika pomwe a Mutharika kudzera kwa owayankhulira awo a Mgeme Kalirani anapangitsa msonkhano… ...