Abambo awiri apezeka akugulitsa chiberekero cha mayi
Abambo awiri ku Ntchisi ali mu chitokosi atapezeka akugulitsa chiberekero cha munthu pa nsika wa Ng’ombe m’bomalo. Mneneri wa a polisi ku Ntchisi a Richard Mwakayoka Kaponda anena kuti anamanga abambo awiriwa patamveka mphekesela kuti… ...