
M’madera am’mphepete mwa nyanja ya Malawi madzi akhonza kusefukira – DCCMS
Nthambi yoona zanyengo m’dziko muno ya Department of Climate Change and Meteorological Services (DCCMS) yachenjeza anthu okhala m’mphepete mwa Nyanja ya Malawi kuti chiopsezo cha kusefukira kwa madzi kwadzidzidzi kukhonza kukwera. Kudzera pa tsamba lake… ...