Namadingo wa ku South Bend, ku mang’ina
Zikukhala ngati oyimba m’dziko muno apeza golide ku America pomwe naye Patience Namadingo watengeka mtima ndi ulendo wa Lulu, ndipo naye wati akupita kukaimba ku South Bend, ku ‘mang'ina' kuja. Posachedwapa, oyimba angapo kuphatikizapo Lawrence… ...