Malamulo a pamseu aja ayamba kuluma: wa minibus amulipilitsa K180,000 chifukwa chonyamula ma 4 – 4
Ukali wa malamulo a pamseu amene aopseza oyendetsa minibus wayamba kuoneka. Bwalo la Milandu mu boma la Mulanje lalamula dalayiva wina wa minibus kuti alipile chindapusa cha K180,000 kapena akagwile ukaidi wa kalavula gaga kwa… ...