Yemwe anali m'modzi mwa akulu akulu ku chipani cha Democratic Progressive DPP a Uladi Mussa ndipo pakali pano adalowa chipani cha Malawi Congress (MCP) ati iwo atafatsa kuwelenga malamulo a chipanichi tsopano ali ndi mangongolomela… ...
Articles By Mphatso Khutcha Richard
Apolisi mu mzinda wa Lilongwe amanga amuna asanu ndi m' modzi chifukwa choba matumba a 78 a mtedza, akina osokera ndi ma sikelo oyezela okwana asanu, zonse za ndalama zokwana 10.8 miliyoni kwacha Malingana ndi… ...
Three Malawian youths who went to Israel to work in farms have been deported to Malawi after they ran away from their farms to seek employment elsewhere. This is according to Lions Recruitment Agency director… ...
Mtsogoleri wa mbali yotsutsa boma wa DPP kunja kwa nyumba ya malamulo a Mary Navicha, ati atengela ku nyumba ya malamulo nkhani yokhudza kalembela wa voti kuti akawunikenso lamulo logwiritsa ntchito chiphaso cha unzika poponya… ...
Yemwe wangosankhidwa kumene kukhala mtsogoleri wa aphungu otsutsa boma wa chipani cha Democratic Progressive (DPP) m'nyumba yamalamulo, mayi Mary Navicha akana kulankhulapo m'nyumbayi pa zomwe mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera analankhula pomwe amatsekulira mkumano wa… ...
Mcdolnad Nginde' Mtetemela has put pen to paper as head coach for newly promoted Super League side Creck Sporting Club. Creck Sporting Club, formerly Kawinga FC, have confirmed the appointment. The coach will be assisted… ...
Dziko la Malawi pamodzi ndi mayiko ena onse padziko lapansi lachiwiri pa 13 Febuluwale limakumbukira nawo tsiku la "Condom'' pamene akatswiri ati a Malawi ambiri sakutha kupeza mwayi wa makondomu mwachangu. M'modzi mwa katswili owona… ...