Bungwe lowona za akatswili pa ukadaulo wa makina a ma kompyuta ndi zipangizo za makono la ICT- Association of Malawi (ICTAM) lati lili lokozeka kuthandiza ndi ukadaulo udziwi wawo ku bungwe lowona za anthu otuluka… ...
Articles By Mphatso Khutcha Richard
Phungu wa wa dela la ku mmwela cha kum'mawa m'boma la Salima a Mike Ng'ombe Mwawa awatulutsa m'nyumba ya malamulo ndipo ati adzabwere pa 13 malichi kamba ka kuyankhula zosayenera mnyumba ya malamulo mu zokambilana… ...
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ati ndi nthawi yabwino tsono kuti makolo azindikire za ubwino okhala ndi ana omwe akhoza kukwanitsa kuwasamala komanso kuwaphunzitsa ndipo ati maphunzilo kuti ayende bwino akuyambila pa zipangizo,… ...
Mighty Mukuru Wanderers Football Club has appointed new members in its supporters' committees to serve for a period of two years. A letter dated 21st February 2024 and signed by board secretary Chancy Gondwe states… ...
Bungwe lolemba nzika la National Registration Bureau (NRB) lati silisinthila a Malawi omwe akufuna kusinthitsa tsiku lobadwa chifukwa tsiku lobadwa pa chiphaso cha nzika ndilotetezedwa. M'malingana ndi chikalata chomwe bungweli latulutsa pa 19 febuluwale chotsimikidwa… ...
Yemwe anali m'modzi mwa akulu akulu ku chipani cha Democratic Progressive DPP a Uladi Mussa ndipo pakali pano adalowa chipani cha Malawi Congress (MCP) ati iwo atafatsa kuwelenga malamulo a chipanichi tsopano ali ndi mangongolomela… ...
Apolisi mu mzinda wa Lilongwe amanga amuna asanu ndi m' modzi chifukwa choba matumba a 78 a mtedza, akina osokera ndi ma sikelo oyezela okwana asanu, zonse za ndalama zokwana 10.8 miliyoni kwacha Malingana ndi… ...