A Malawi onse amene anagwidwa mu dziko la South Africa kamba kopita mu dzikomo opanda chilolezo ndipo akusungidwa pa malo a Lindela kudikila kubwela mu dziko lino ayiwale kuti abwela msanga. Izi zadziwika pamene a… ...
Articles By Lindiwe Sambalikagwa
A Malawi apemphedwa kuti akhale anthu omvetsetsa pa nkhani ya lamulo lokhudzana ndi kuchotsa mimba. Malingana ndi mkulu wa bungwe loona kuti palibe kusiyana pakati pa akazi ndi amuna, la Gender Coordination Network, Mayi Emma… ...
Malawi’s renowned Evangelist Shadreck Wame has been killed by unknown people at his house in Salima district, reports that Malawi24 is following say. Reports say Wame was found dead in his house, which was broken into… ...
Inu nonse amene mukutchukitsa kuti mtsogoleri wa dziko lino akudwala ndipo akuganiza zotula pansi udindo, akuti muzimangidwa. Anthu ena omenyela ufulu wa anthu wa chibadwidwe ndiwo apempha boma la Malawi kuti liyambe kuunika bwino nkhani… ...
Pataphulika mphekesera zoti mtsogoleri wa dziko lino anachedwa mu dziko la Amereka kamba koti anagonekedwa ku chipatala, mkuluyu ali ndi mwai otsitsa nkhani zimenezo lero mwa yekha. Malingana ndi a kunyumba ya boma ku Lilongwe,… ...
Malawi President Peter Mutharika needs to hold his celebrations on the award from the International Royal Academy, as fresh revelations show that the organisation does not fall under the United Nations (UN) as it is… ...
Malawi President Peter Mutharika returns home this Sunday, a revelation that has come in the wake of trending speculations that he had fallen into coma. A press statement from the State House as signed by… ...