Kodi mwaona kale kuti nyumba zanu ndi zodalilika? Ndiye kuli zimbudzi, zija zimangogwa ndi Mvula, munamanga zolimba? Bungwe loona za nyengo mu dziko muno lanena kuti a Malawi akhale okonzeka chifukwa Mvula ya mphamvu ikuyembekezeleka… ...
Articles By Kondwani Mkhalipi-Manyungwa
Nkutheka kuti inu simunamwepo koma mwina azanu munakhisana nawo aja anamwapo. Madzi atubvi la khatikhati anavuta ku Lilongwe aja atulukiranso. Pano ndiye adza ndi ukali, kununkha kwakeko ndiye ngati wangowatunga mu suweji madziwa kuti umwe.… ...
Pa ngodya zitatu za chipani cholamula cha DPP chija, imodzi ndiye ikukhala ngati ikuvutilapo. Anthu akugonabe ndi mantha, Chitetezo ndi kumpanda wachifumu kokha basi. Anthu a mmudzi mwa Goma m’boma la Chikhwawa akukhala mwa mantha… ...
A PP kodi mulipo? Pitani ku maofesi a chipani chanu chifukwa Mtsogoleri wanu ati akubwera ndipo 2019 akhala akupikisana nawo pa chisankho. Malinga ndi malipoti a olemba nkhani, Mayi Banda alengeza zoti azapikisana nawo pa… ...
The secret dealings between the ruling Democratic Progressive Party (DPP) and the opposition People's Party (PP) will not last long and will not carry on to the 2019 polls. Former President Joyce Banda has announced… ...
Iran coach Carlos Queiroz believes Barcelona and Argentinean legend Lionel Messi is too good for a human being and has asked FIFA to investigate superstar striker if he is indeed human. Queiroz is so stunned by the… ...
Ululu wa Vita ukuzunguzabe Manoma. Mbwiza anavina Manoma ku Congo, Tchopa wa pa Bingu adakawazunguzabe a ku banja la nyerere. Inu, Vita si zibwana iyayi. Ndi izi lero Manoma ali ngati pa nsanja ya Babulo… ...