
Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino Flames lero pa 26 March ikuyembekezereka kuthambitsana ndi Chipolopolo ya m'dziko la Zambia kulimbirana malo achitatu mu 4 Nations Tournament ndipo masewero ake ayamba 2 koloko masana.… ...